Olemba: Burnett Munthali Dr. Sanned Lubani, yemwe ndi mtsogoleri wa Seventh-day Adventist Church (SDA) m’dera la Eastern Malawi Conference, wayankhula mwamphamvu ponena za kufunika kolimbikitsa ubale ...